Hymn 960 Tilikupita kwathu kuja treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 960 Tilikupita kwathu kuja Tilikupita kwathu kuja Munjira ya atate athu, Amakondwera lero lomwe; Tinka kuonana nawo.