Hymn 952 Ndimayenda paulendo, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 952 Ndimayenda paulendo, Ndimayenda paulendo, Ndi yaminga njira yake; Tsoka ndikapeza, koma Ndinka kwa Atate; Pena m’mtima mwanga mwada, Pena andibvuta ‘dani, Ndikatenga nkhawa, mantha, Amadziwako.