Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 94 Ndani anatiwombola?
Ndani anatiwombola?
Mwana wa Mulungu pa mtanda,
Anatani?
Anafera.
Ali kuti?
Akhaladi m’Mwamba
kutipempherera.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 94 Ndani anatiwombola?
Ndani anatiwombola?
Mwana wa Mulungu pa mtanda,
Anatani?
Anafera.
Ali kuti?
Akhaladi m’Mwamba
kutipempherera.