Hymn 917 Ndi nkhondo ikaleka treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 917 Ndi nkhondo ikaleka Ndi nkhondo ikaleka Kwa Mulungu komweko, Ndi ukapolo watha, Udani wathanso; Ndi zakuopsa zonse Ndi zosauka zii! Ndi mwayi wa kwa Mlungu Udzaza mutu tho!