Hymn 90 Ufuna kuleka kunyadako? treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 90 Ufuna kuleka kunyadako? Ufuna kuleka kunyadako? Ilipo mphamvu m’mwazi wake; Idzatu pa mtanda nutsukidwe, Muli mphamvu m’mwazi wake.