Hymn 893 Mtima wanga ndikonzera, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 893 Mtima wanga ndikonzera, Mtima wanga ndikonzera, Mbuye Yesu aitana; Ati: “Mwana, tapemphera, Ine sindidzakukana.”