Hymn 863 A! maliro m’Mpingo mwanu kulirira ‘balewo treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 863 A! maliro m’Mpingo mwanu kulirira ‘balewo A! maliro m’Mpingo mwanu kulirira ‘balewo Adasokerera kale ndi zoipa zapa dziko. Muwabwezerenso kwanu kuti akakhale mommo.