Hymn 861 Mbuye, Mpingo wanu usauka kwa kukuludi; treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 861 Mbuye, Mpingo wanu usauka kwa kukuludi; Mbuye, Mpingo wanu usauka kwa kukuludi; Kale lija munatsitsa Mzimu wanu Wakuyera; Lero linonso muchite, ulimbike Mpingo wanu.