Hymn 847 Konse kuli mdima bii treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 847 Konse kuli mdima bii Konse kuli mdima bii Kosakhala Inutu; Nlosakondwa tsikuli Mosawala Inu ‘mu. Ndionetu m’katimo Mwakuwala kwanuko.