Hymn 803 Mulungu wanga, Dzuwatu treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 803 Mulungu wanga, Dzuwatu Mulungu wanga, Dzuwatu La mtima wanga ndinudi; Palibe mdima ngatitu Mukawalira inedi.