Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 797 Kwacha lero kwati mbee,
Kwacha lero kwati mbee,
Tsikku la Mulunguli;
Dzuwa liwaliradi
Thambo ndi zapansipa;
Upumira mpweyawu
Wa Mulungu konseku.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 797 Kwacha lero kwati mbee,
Kwacha lero kwati mbee,
Tsikku la Mulunguli;
Dzuwa liwaliradi
Thambo ndi zapansipa;
Upumira mpweyawu
Wa Mulungu konseku.