Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 792 Dzuwa la Mulungu
Dzuwa la Mulungu
Ladzatu labwino;
Ndi chimwemwe ife
Tiliona lero.
Lithawitsa nkhawa,
Lichotsanso mantha,
Ndimo m’mtima mwathu
Likhalitsa bata.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 792 Dzuwa la Mulungu
Dzuwa la Mulungu
Ladzatu labwino;
Ndi chimwemwe ife
Tiliona lero.
Lithawitsa nkhawa,
Lichotsanso mantha,
Ndimo m’mtima mwathu
Likhalitsa bata.