Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 789 Ndi lokoma m’Mwambamo,
Ndi lokoma m’Mwambamo,
Mbuye, Bwalo lanulo;
Ndi mwabwino muli ‘Nu
Dziko losachimwali;
Mtima wanga wonsewu
Umakhumba m’Mwambamo
Nkhope ya Mbuyathuyu,
Mlungu wa chisomoyo.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 789 Ndi lokoma m’Mwambamo,
Ndi lokoma m’Mwambamo,
Mbuye, Bwalo lanulo;
Ndi mwabwino muli ‘Nu
Dziko losachimwali;
Mtima wanga wonsewu
Umakhumba m’Mwambamo
Nkhope ya Mbuyathuyu,
Mlungu wa chisomoyo.