Hymn 779 Yesu Mbuye wanga, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 779 Yesu Mbuye wanga, Yesu Mbuye wanga, Mkhale m’mtima mwanga, Ndiwotu kachisi wanu. Ikafika imfa, Mundisunge kwanu Kuli Inu ndi angelo. Moyo wanga ulimbike Kufikira ine Ndidzakupenyani.