Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 771 Tsopano alandira
Tsopano alandira
Chizindikiro chanu
Munachiika ndinu
Cha Ubatizo wanu.
Mulembe Dzina lanu
M’mitima mwa onsewa;
M’wabatizenso Mbuye,
Ndi Mzimu Wakuyera.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 771 Tsopano alandira
Tsopano alandira
Chizindikiro chanu
Munachiika ndinu
Cha Ubatizo wanu.
Mulembe Dzina lanu
M’mitima mwa onsewa;
M’wabatizenso Mbuye,
Ndi Mzimu Wakuyera.