Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 741 Chakudya ichi chidzapita du,
Chakudya ichi chidzapita du,
Chizindikitsa za Kumwambazo;
Zosapitazo tidzalawatu,
Za Yesu mwini wakukondako.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 741 Chakudya ichi chidzapita du,
Chakudya ichi chidzapita du,
Chizindikitsa za Kumwambazo;
Zosapitazo tidzalawatu,
Za Yesu mwini wakukondako.