Hymn 69 Kwathu sipadziko, ndingopitirira, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 69 Kwathu sipadziko, ndingopitirira, Kwathu sipadziko, ndingopitirira, Ndadzikundikira chumaKumwambako; Mngelo akodola pakhomo lam’mwamba; Ndipo dziko lapansi sindyesa kwathu.