Hymn 688 Anthu akum’mawa treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 688 Anthu akum’mawa Anthu akum’mawa Nanka msangako, Nzure ‘nali nazo, Nafatsansowo; Nanka kuli Mwana Anabadwayo; Anatsogozedwa Ndi nyenyeziyo.