Hymn 669 Anyamata limikani, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 669 Anyamata limikani, Anyamata limikani, Gwirani nkhondoyi; Yesu salephera mwini, Satiiwalira ‘yi.