Hymn 663 Anyamata a Mulungu, treasurehymns 9 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 663 Anyamata a Mulungu, Anyamata a Mulungu, Muzigwira nkhondoyo, Mumenyane ndi Satana Mzimu wakunyengayo.