Hymn 660 Tumizani kuunikako, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 660 Tumizani kuunikako, Tumizani kuunikako, Kuoneketu kwa onsewo; Tumizani kuunikako, Nthawi zonsedi kuwaletu.