Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 648 Mulungu wa Kumwamba,
Mulungu wa Kumwamba,
Tabwera kunoku
Ndi mtima wokondwera
Kulowa m’nyumbayi;
Chifukwa cha zabwino
Mwatichitirazi
Tikukuyamikirani.
Leroli.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 648 Mulungu wa Kumwamba,
Mulungu wa Kumwamba,
Tabwera kunoku
Ndi mtima wokondwera
Kulowa m’nyumbayi;
Chifukwa cha zabwino
Mwatichitirazi
Tikukuyamikirani.
Leroli.