Site icon Treasure Hymns – Chichewa

Hymn 647 Tiyamike Mlungu ‘Tate,

Chichewa Believers Christian Hymns

Hymn 647 Tiyamike Mlungu ‘Tate,

 

Tiyamike Mlungu ‘Tate,

Tiyamike Mwanayo,

Tiyamike Mzimu wake,

Onse omwe Mmodzitu,

Waulemerero wonse

Ndi wamphamvu ponsepo.

Exit mobile version