Hymn 629 Tinayenda muli mdima treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 629 Tinayenda muli mdima Tinayenda muli mdima Wotidetsa nkhawawo, Pena tinangosauka Ndi zobvuta zathuzo; Koma Inu munalimo Mumitambo yomweyo, Nafe tinathandizana Ndi mdalitso wanuwo.