Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 622 Tiyamikira ‘Tate,
Tiyamikira ‘Tate,
Zabwino zonse zino,
Kubzala ndi kukunkha
Ndi moyo tili nawo.
Kuninkha Inu Mbuye
tilibe mtulo wina,
Komatu tipereka
Mitima yoyamika.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 622 Tiyamikira ‘Tate,
Tiyamikira ‘Tate,
Zabwino zonse zino,
Kubzala ndi kukunkha
Ndi moyo tili nawo.
Kuninkha Inu Mbuye
tilibe mtulo wina,
Komatu tipereka
Mitima yoyamika.