Hymn 610 Nafenso tidzadzuka kwa ‘ke ngati maluwawo, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 610 Nafenso tidzadzuka kwa ‘ke ngati maluwawo, Nafenso tidzadzuka kwa ‘ke ngati maluwawo, Timlambire Mbuye; Oyera mtima adzabvala mbuu! Pakudza Kristuyo, Timgwadiretu.