Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 594 Monga may’ asusuza
Monga may’ asusuza
Mwana wake polira,
Wakunditonthozatu
Ndinu, munditonthoze,
Inde, m’njira yanuyi
Munditsogoleretu.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 594 Monga may’ asusuza
Monga may’ asusuza
Mwana wake polira,
Wakunditonthozatu
Ndinu, munditonthoze,
Inde, m’njira yanuyi
Munditsogoleretu.