Hymn 59 Tinachoka munjira ya imfa, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 59 Tinachoka munjira ya imfa, Tinachoka munjira ya imfa, Nanga inu? Nanga inu? Takopeka ndi Mawu a Yesu; Nanga inu?