Hymn 571 Kwa ife lero anabadwa treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 571 Kwa ife lero anabadwa Kwa ife lero anabadwa Mwana wa Mariyayo, Pamsinkhu, inde mn’gono koma Mwini dziko lonseli.