Hymn 569 Tiimbe ndi kulalikira treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 569 Tiimbe ndi kulalikira Tiimbe ndi kulalikira Mthenga wa chikondicho Anamva Mlungu m’Mwambamo Kulira kwathu pansipa.