Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 565 Koma sitimpenya m’khola
Koma sitimpenya m’khola
Muli ng’ombe momwemo;
Ayi, tidzamwona m’Mwamba
Muli Mlungu ‘Tatewo.
Ana akuyera mbuu
Adzamzunguliratu.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 565 Koma sitimpenya m’khola
Koma sitimpenya m’khola
Muli ng’ombe momwemo;
Ayi, tidzamwona m’Mwamba
Muli Mlungu ‘Tatewo.
Ana akuyera mbuu
Adzamzunguliratu.