Hymn 564 Ndi chifukwa atikonda, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 564 Ndi chifukwa atikonda, Ndi chifukwa atikonda, Tidzampenya masowa, Kuti Mwanayo wofatsa Ndiye mwini m’Mwambamo; Atengera ana ake Komwe adapitako.