Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 524 Wokoma Mbuyathu
Wokoma Mbuyathu
kwitana ana onse;
Atsalanso ambiri ena
sanamvera zake;
Sanamva mawu akewo,
Sadziwa kuti ‘natinso;
“Lolani ana abwere kwa Ine,
Lolani ana abwere kwa Ine.”
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 524 Wokoma Mbuyathu
Wokoma Mbuyathu
kwitana ana onse;
Atsalanso ambiri ena
sanamvera zake;
Sanamva mawu akewo,
Sadziwa kuti ‘natinso;
“Lolani ana abwere kwa Ine,
Lolani ana abwere kwa Ine.”