Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 523 “Ndidzawalandira,
“Ndidzawalandira,
k’wasunga m’manja mwanga;
Ndi Mbusa wao Inetu,
msachotse ana anga;
Akandipatsa mtimawo,
Adzanka ndine Kwathuko;
Lolani ana abwere kwa Ine,
Lolani ana abwere kwa Ine.”
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 523 “Ndidzawalandira,
“Ndidzawalandira,
k’wasunga m’manja mwanga;
Ndi Mbusa wao Inetu,
msachotse ana anga;
Akandipatsa mtimawo,
Adzanka ndine Kwathuko;
Lolani ana abwere kwa Ine,
Lolani ana abwere kwa Ine.”