Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 521 Apunzitsi, ana omwe,
Apunzitsi, ana omwe,
Ndi akulu, t’iimbe tonse;
Nyimbo zathu zidzakwera
Zikamveke m’Mwamba monse.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 521 Apunzitsi, ana omwe,
Apunzitsi, ana omwe,
Ndi akulu, t’iimbe tonse;
Nyimbo zathu zidzakwera
Zikamveke m’Mwamba monse.