Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 520 Tamva tikondane naye,
Tamva tikondane naye,
Tiwerenge Mawu ake,
M’njira mwake tiyendemo,
Tiziimba nyimbo zake.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 520 Tamva tikondane naye,
Tamva tikondane naye,
Tiwerenge Mawu ake,
M’njira mwake tiyendemo,
Tiziimba nyimbo zake.