Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 515 Kuphiri la ‘Zitona,
Kuphiri la ‘Zitona,
Mumpingo wa ‘nthuwo,
‘Namkupizira mnjedza
Naimba nyimboyo.
Angelo akumwambako
Napokerezanso;
“Osana m’Mwambamwamba
Kwa Mlungu wathuyo.”
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 515 Kuphiri la ‘Zitona,
Kuphiri la ‘Zitona,
Mumpingo wa ‘nthuwo,
‘Namkupizira mnjedza
Naimba nyimboyo.
Angelo akumwambako
Napokerezanso;
“Osana m’Mwambamwamba
Kwa Mlungu wathuyo.”