Hymn 514 Osanatu, osana, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 514 Osanatu, osana, Osanatu, osana, ‘Naimba anawo; M’kachisi wa Mulungu Mwamveka nyimboyo. ‘Nalemekeza Yesuyo Wak’wadalitsayo; Anamuyamikira M’ubwana wawowo.