Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 508 Mzimu Woyera akhala mwa ine,
Mzimu Woyera akhala mwa ine,
Atsimikiza chikondi cha Yesu;
Ine n’tachimwa amandikumbutsa;
“Lapa mwana ‘we, akukonda Yesu,”
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 508 Mzimu Woyera akhala mwa ine,
Mzimu Woyera akhala mwa ine,
Atsimikiza chikondi cha Yesu;
Ine n’tachimwa amandikumbutsa;
“Lapa mwana ‘we, akukonda Yesu,”