Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 502 Ndikonda mbiri yomwe
Ndikonda mbiri yomwe
Ya amithengawo
Ya Mbuye, Mfumu yathu
Pofika pansipa;
Zochimwa zindizinga,
Koma ndidziwatu
Anawombola ine
Pakundikondadi.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 502 Ndikonda mbiri yomwe
Ndikonda mbiri yomwe
Ya amithengawo
Ya Mbuye, Mfumu yathu
Pofika pansipa;
Zochimwa zindizinga,
Koma ndidziwatu
Anawombola ine
Pakundikondadi.