Hymn 50 Akhristu nyamulani treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 50 Akhristu nyamulani Akhristu nyamulani Maneno a Mulungu, Ndi moyo lalikani Pa dziko lonselo; Ndi Yesu Mpulumutsi Anatiferatu; Adzabvomera onse: Ndi Mwana wa Mlungu.