Hymn 493 Ndimalira kwa Inutu, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 493 Ndimalira kwa Inutu, Ndimalira kwa Inutu, Mpatse mtimawo wabwino; M’Dziko lanu lowalalo Mulandire mwana wanu.