Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 49 Ndi ife akudziwa
Ndi ife akudziwa
Chikondi cha Mlungu,
Kodi tidzawamana
Kuwala kwa Ktistu?
Chipulumutso! Inde,
Tichibukitsetu,
Kuti mitundu yonse
Ibwere kwa Yesu.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 49 Ndi ife akudziwa
Ndi ife akudziwa
Chikondi cha Mlungu,
Kodi tidzawamana
Kuwala kwa Ktistu?
Chipulumutso! Inde,
Tichibukitsetu,
Kuti mitundu yonse
Ibwere kwa Yesu.