Hymn 457 Palibe mwana wakuchepa treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 457 Palibe mwana wakuchepa Palibe mwana wakuchepa Kunyamula mtandawu; Ambuye Yesu mutipatse Mtima wokondanatu.