Hymn 454 Kapena m’mtima ndimakwiya, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 454 Kapena m’mtima ndimakwiya, Kapena m’mtima ndimakwiya, Nditukwana mnzangayo, Kapena ndidzitama – izi Ndilekere Mbuyeyo.