Site icon Treasure Hymns – Chichewa

Hymn 45 Malawi dziko lokongola,

Chichewa Believers Christian Hymns

Hymn 45 Malawi dziko lokongola,

 

Malawi dziko lokongola,

La chonde ndi ufulu,

Nyanja ndi mphepo ya m’mapiri,

Ndithudi tadala;

Zigwa, mapiri, nthaka, dzinthu,

Mphatso zaulere;

Nkhalango, madambo abwino,

Ngwokoma Malawi.

Exit mobile version