Hymn 44 Mlungu dalitsani Malawi, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 44 Mlungu dalitsani Malawi, Mlungu dalitsani Malawi, Mumsunge m’mtendere; Gonjetsani adani onse, Njala, nthenda, nsanje; Luzitsani mitima yathu Kuti tisaope, Mdalitse Mtsogoleri, nafe, Ndi Mayi Malawi.