Hymn 439 Nthawi yaubwana yatha, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 439 Nthawi yaubwana yatha, Nthawi yaubwana yatha, Sukulu yathu yathanso; Nkhawa ndi zowawa zomwe Zitibisaliranso.