Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 429 Haya! Tipitenso
Haya! Tipitenso
M’njira yomwe ija
Ana a Mulungu
Onse adaponda.
Tizisiya zonse,
tiziyenda msanga,
Tisamachewuka
Mpaka tapambana.
Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 429 Haya! Tipitenso
Haya! Tipitenso
M’njira yomwe ija
Ana a Mulungu
Onse adaponda.
Tizisiya zonse,
tiziyenda msanga,
Tisamachewuka
Mpaka tapambana.