Hymn 420 Mtima umabisala treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 420 Mtima umabisala Mtima umabisala M’manja mwa Yesumu; Mbuye, musunge ine, Munandifera ‘ne. Ndilinda mopirira Mpaka wachoka mdima. Ndikaonana naye Yesu Ambuye wanga.